Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:21 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, ptsa. 18-191/1/2000, ptsa. 14-16 Yesaya 2, ptsa. 319-320
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+