Yesaya 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinapondaponda mitundu ya anthu mu mkwiyo wanga, ndipo ndinawaledzeretsa ndi ukali wanga.+ Ndinachititsa kuti magazi awo atuluke mwamphamvu n’kutayikira pansi.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:6 Yesaya 2, ptsa. 353-354
6 Ndinapondaponda mitundu ya anthu mu mkwiyo wanga, ndipo ndinawaledzeretsa ndi ukali wanga.+ Ndinachititsa kuti magazi awo atuluke mwamphamvu n’kutayikira pansi.”+