Yesaya 63:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ali kuti amene anachititsa mkono wake wokongola+ kupita kudzanja lamanja la Mose, amene anagawanitsa madzi pamaso pawo+ kuti adzipangire dzina lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:12 Yesaya 2, ptsa. 357-358
12 Ali kuti amene anachititsa mkono wake wokongola+ kupita kudzanja lamanja la Mose, amene anagawanitsa madzi pamaso pawo+ kuti adzipangire dzina lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+