Yesaya 65:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:3 Yesaya 2, ptsa. 374-375
3 anthu amene akundichitira mwano+ nthawi zonse m’maso muli gwa! Amene amapereka nsembe m’minda,+ amene amafukiza nsembe zautsi+ panjerwa,