Yesaya 65:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo amanena kuti, ‘Khala pawekha. Usandiyandikire, kuti ndingakupatsire chiyero changa.’+ Iwo ali ngati utsi m’mphuno mwanga,+ ngati moto woyaka tsiku lonse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:5 Yesaya 2, ptsa. 374-375
5 Iwo amanena kuti, ‘Khala pawekha. Usandiyandikire, kuti ndingakupatsire chiyero changa.’+ Iwo ali ngati utsi m’mphuno mwanga,+ ngati moto woyaka tsiku lonse.+