Yesaya 65:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wanena kuti: “Monga momwe vinyo watsopano+ amapezekera m’tsango la mphesa ndipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge,+ pakuti muli dalitso mmenemu,’+ inenso ndidzachita zomwezo chifukwa cha atumiki anga, kuti ndisawawononge onse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:8 Yesaya 2, ptsa. 376-377
8 Yehova wanena kuti: “Monga momwe vinyo watsopano+ amapezekera m’tsango la mphesa ndipo wina amanena kuti, ‘Musaliwononge,+ pakuti muli dalitso mmenemu,’+ inenso ndidzachita zomwezo chifukwa cha atumiki anga, kuti ndisawawononge onse.+