Yesaya 65:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa Yakobo ndidzatulutsamo mwana,+ ndipo mwa Yuda ndidzatulutsamo yemwe adzalandire cholowa cha mapiri anga.+ Anthu anga osankhidwa mwapadera adzapatsidwa dziko lamapirilo,+ ndipo atumiki anga adzakhala mmenemo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:9 Yesaya 2, ptsa. 376-377
9 Mwa Yakobo ndidzatulutsamo mwana,+ ndipo mwa Yuda ndidzatulutsamo yemwe adzalandire cholowa cha mapiri anga.+ Anthu anga osankhidwa mwapadera adzapatsidwa dziko lamapirilo,+ ndipo atumiki anga adzakhala mmenemo.+