Yesaya 65:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atumiki anga adzafuula mokondwa chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,+ koma inuyo mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima ndipo mudzafuula chifukwa chosweka mtima.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:14 Yesaya 2, ptsa. 379-380
14 Atumiki anga adzafuula mokondwa chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,+ koma inuyo mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima ndipo mudzafuula chifukwa chosweka mtima.+