Yesaya 65:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Mmbulu+ ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi.+ Mkango udzadya udzu ngati ng’ombe yamphongo,+ ndipo njoka izidzadya fumbi.+ Zimenezi sizidzapweteka aliyense+ kapena kuwononga chilichonse m’phiri langa lonse loyera,”+ watero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:25 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, ptsa. 9-104/15/2000, ptsa. 17-18 Yesaya 2, tsa. 388 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 174-175
25 “Mmbulu+ ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi.+ Mkango udzadya udzu ngati ng’ombe yamphongo,+ ndipo njoka izidzadya fumbi.+ Zimenezi sizidzapweteka aliyense+ kapena kuwononga chilichonse m’phiri langa lonse loyera,”+ watero Yehova.
65:25 Nsanja ya Olonda,9/15/2012, ptsa. 9-104/15/2000, ptsa. 17-18 Yesaya 2, tsa. 388 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 174-175