Yeremiya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo poti wachita zinthu zonsezi, ine ndinamupempha mobwerezabwereza kuti abwerere kwa ine, koma iye sanabwerere.+ Ndipo Yuda anali kungoyang’anitsitsa zimene m’bale wake wachinyengoyo anali kuchita.+
7 Pambuyo poti wachita zinthu zonsezi, ine ndinamupempha mobwerezabwereza kuti abwerere kwa ine, koma iye sanabwerere.+ Ndipo Yuda anali kungoyang’anitsitsa zimene m’bale wake wachinyengoyo anali kuchita.+