Yeremiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo mudzabalana ndi kuchuluka m’dzikoli masiku amenewo,” watero Yehova.+ “Iwo sadzafuulanso kuti, ‘Likasa la pangano la Yehova!’+ Sadzaliganiziranso m’mitima yawo, kulikumbukira,+ kapena kulilakalaka ndipo sadzapanganso likasa lina.
16 Pamenepo mudzabalana ndi kuchuluka m’dzikoli masiku amenewo,” watero Yehova.+ “Iwo sadzafuulanso kuti, ‘Likasa la pangano la Yehova!’+ Sadzaliganiziranso m’mitima yawo, kulikumbukira,+ kapena kulilakalaka ndipo sadzapanganso likasa lina.