Yeremiya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 108/15/1998, tsa. 6
5 Yehova wanena kuti: “Wotembereredwa ndi munthu aliyense wokhulupirira mwa munthu aliyense wochokera kufumbi.+ Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za dzanja la munthu,+ komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.+
17:5 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 44 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 108/15/1998, tsa. 6