Yeremiya 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova wandiuza kuti: “Pita ukaime pachipata cha ana a anthu pamene mafumu a Yuda amalowera ndi kutulukira. Kenako ukaimenso pazipata zina zonse za Yerusalemu.+
19 Yehova wandiuza kuti: “Pita ukaime pachipata cha ana a anthu pamene mafumu a Yuda amalowera ndi kutulukira. Kenako ukaimenso pazipata zina zonse za Yerusalemu.+