Yeremiya 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘“Ndipo mukadzandimvera,”+ watero Yehova, “mwa kusalowa ndi katundu pazipata za mzindawu pa tsiku la sabata+ ndi kuona tsiku la sabata kukhala lopatulika mwa kusagwira ntchito iliyonse pa tsikuli,+
24 “‘“Ndipo mukadzandimvera,”+ watero Yehova, “mwa kusalowa ndi katundu pazipata za mzindawu pa tsiku la sabata+ ndi kuona tsiku la sabata kukhala lopatulika mwa kusagwira ntchito iliyonse pa tsikuli,+