-
Yeremiya 29:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Awa ndi mawu a m’kalata imene mneneri Yeremiya anatumiza kuchokera ku Yerusalemu kupita kwa akuluakulu otsala pakati pa anthu amene anali ku ukapolo, kwa ansembe ndi kwa aneneri. Kalatayi inapitanso kwa anthu onse amene Nebukadinezara anawatenga kupita nawo ku ukapolo ku Babulo kuchokera ku Yerusalemu.+
-