Yeremiya 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndikutumizira anthu amene anatsala ku Yuda lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri+ ndipo ndidzawachititsa kukhala ngati nkhuyu zophulika zimene munthu sangazidye chifukwa cha kuipa kwake.”’+
17 ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndikutumizira anthu amene anatsala ku Yuda lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri+ ndipo ndidzawachititsa kukhala ngati nkhuyu zophulika zimene munthu sangazidye chifukwa cha kuipa kwake.”’+