Yeremiya 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Choncho nonsenu amene muli ku ukapolo,+ amene ndinakuchotsani ku Yerusalemu ndi kukutumizani ku Babulo, imvani mawu awa a Yehova.+
20 “Choncho nonsenu amene muli ku ukapolo,+ amene ndinakuchotsani ku Yerusalemu ndi kukutumizani ku Babulo, imvani mawu awa a Yehova.+