Yeremiya 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 N’chifukwa chake iye watitumizira kalata ku Babulo kuno yonena kuti: “Mukhala akapolo kumeneko kwa nthawi yaitali. Mangani nyumba ndi kukhalamo. Limani minda ndi kudya zipatso zake,+ . . .”’”’”
28 N’chifukwa chake iye watitumizira kalata ku Babulo kuno yonena kuti: “Mukhala akapolo kumeneko kwa nthawi yaitali. Mangani nyumba ndi kukhalamo. Limani minda ndi kudya zipatso zake,+ . . .”’”’”