Yeremiya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.