Yeremiya 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu mitundu ya anthu, imvani mawu a Yehova, ndipo mulengeze mawuwo pazilumba zakutali,+ kuti: “Amene wamwaza Isiraeli ndiye adzamusonkhanitsanso+ ndipo adzamusunga mmene m’busa amasungira nkhosa zake.+
10 Inu mitundu ya anthu, imvani mawu a Yehova, ndipo mulengeze mawuwo pazilumba zakutali,+ kuti: “Amene wamwaza Isiraeli ndiye adzamusonkhanitsanso+ ndipo adzamusunga mmene m’busa amasungira nkhosa zake.+