Yeremiya 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi udzapatukira uku ndi uku kufikira liti,+ iwe mwana wamkazi wosakhulupirika?+ Yehova walenga chinthu chatsopano padziko lapansi. Chinthucho n’chakuti, mkazi wamba adzakupatira mwamuna wamphamvu.”
22 Kodi udzapatukira uku ndi uku kufikira liti,+ iwe mwana wamkazi wosakhulupirika?+ Yehova walenga chinthu chatsopano padziko lapansi. Chinthucho n’chakuti, mkazi wamba adzakupatira mwamuna wamphamvu.”