Yeremiya 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo Yuda ndi mizinda yake yonse adzakhala pamodzi m’dzikolo. Mudzakhalanso alimi ndi anthu oweta ziweto.+
24 Ndipo Yuda ndi mizinda yake yonse adzakhala pamodzi m’dzikolo. Mudzakhalanso alimi ndi anthu oweta ziweto.+