Yeremiya 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu amenewa ndidzawapereka m’manja mwa adani awo ndi m’manja mwa onse ofuna moyo wawo.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka m’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.+
20 Anthu amenewa ndidzawapereka m’manja mwa adani awo ndi m’manja mwa onse ofuna moyo wawo.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha zolengedwa zouluka m’mlengalenga ndi zilombo zakutchire.+