Yeremiya 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+
20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+