Yeremiya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero Ebedi-meleki anatenga amunawo ndipo iye analowa m’nyumba ya mfumu, kumunsi kwa malo osungirako chuma.+ Kumeneko anatenga nsanza ndi zidutswa zotha ntchito zansalu. Zimenezi anazitsitsira m’chitsime kwa Yeremiya+ pogwiritsa ntchito zingwe. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:11 Nsanja ya Olonda,5/1/2012, tsa. 31
11 Chotero Ebedi-meleki anatenga amunawo ndipo iye analowa m’nyumba ya mfumu, kumunsi kwa malo osungirako chuma.+ Kumeneko anatenga nsanza ndi zidutswa zotha ntchito zansalu. Zimenezi anazitsitsira m’chitsime kwa Yeremiya+ pogwiritsa ntchito zingwe.