Yeremiya 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Yeremiya anauza Zedekiya kuti: “Kodi ndikakuuzani simundipha? Komanso ndikakulangizani, simundimvera ayi.”+
15 Pamenepo Yeremiya anauza Zedekiya kuti: “Kodi ndikakuuzani simundipha? Komanso ndikakulangizani, simundimvera ayi.”+