Yeremiya 38:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Patapita nthawi, akalonga onse anafika kwa Yeremiya ndipo anayamba kumufunsa mafunso. Yeremiya anawayankha mogwirizana ndi mawu onsewa amene mfumu inamulamula.+ Choncho akalongawo anakhala chete pamaso pake chifukwa sanamve zimene anakambirana.
27 Patapita nthawi, akalonga onse anafika kwa Yeremiya ndipo anayamba kumufunsa mafunso. Yeremiya anawayankha mogwirizana ndi mawu onsewa amene mfumu inamulamula.+ Choncho akalongawo anakhala chete pamaso pake chifukwa sanamve zimene anakambirana.