Yeremiya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ananena za tsoka limeneli moti anatsimikiza kukwaniritsa zimene ananenazo. Anatero chifukwa anthu inu munachimwira Yehova ndipo simunamvere mawu ake. Choncho monga mmene ukuoneramu, zimenezi zachitikadi.+
3 Yehova ananena za tsoka limeneli moti anatsimikiza kukwaniritsa zimene ananenazo. Anatero chifukwa anthu inu munachimwira Yehova ndipo simunamvere mawu ake. Choncho monga mmene ukuoneramu, zimenezi zachitikadi.+