Yeremiya 41:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma anthuwo atafika pakati pa mzinda, Isimaeli mwana wa Netaniya anawapha ndi kuwaponya m’chitsime. Iye anapha anthuwa mothandizana ndi amuna amene anali naye.+
7 Koma anthuwo atafika pakati pa mzinda, Isimaeli mwana wa Netaniya anawapha ndi kuwaponya m’chitsime. Iye anapha anthuwa mothandizana ndi amuna amene anali naye.+