Yeremiya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.
11 Patapita nthawi, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo+ amene anali naye anamva zoipa zonse zimene Isimaeli mwana wa Netaniya anachita.