-
Yeremiya 41:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno anthu onse amene anali ndi Isimaeli ataona Yohanani mwana wa Kareya ndi akuluakulu onse a magulu ankhondo amene anali naye, anayamba kusangalala kwambiri.
-