Yeremiya 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu onse amene Isimaeli anawagwira ku Mizipa+ anatembenuka ndi kuthawira kwa Yohanani mwana wa Kareya.
14 Anthu onse amene Isimaeli anawagwira ku Mizipa+ anatembenuka ndi kuthawira kwa Yohanani mwana wa Kareya.