Yeremiya 43:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero Yohanani mwana wa Kareya, akuluakulu onse a magulu ankhondo ndi anthu onse sanamvere mawu a Yehova+ kuti apitirize kukhala m’dziko la Yuda,+
4 Chotero Yohanani mwana wa Kareya, akuluakulu onse a magulu ankhondo ndi anthu onse sanamvere mawu a Yehova+ kuti apitirize kukhala m’dziko la Yuda,+