Yeremiya 44:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Izi zachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene mwachita ndi kundikhumudwitsa nazo. Mwafukiza nsembe zautsi+ ndi kutumikira milungu ina imene inu kapena makolo anu simunaidziwe.+
3 Izi zachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene mwachita ndi kundikhumudwitsa nazo. Mwafukiza nsembe zautsi+ ndi kutumikira milungu ina imene inu kapena makolo anu simunaidziwe.+