Yeremiya 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mwaiwala zoipa zimene makolo anu anachita?+ Kodi mwaiwala zoipa za mafumu a Yuda+ ndi za akazi awo,+ zoipa zanu ndi za akazi anu,+ zimene munachita m’dziko la Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu?
9 Kodi mwaiwala zoipa zimene makolo anu anachita?+ Kodi mwaiwala zoipa za mafumu a Yuda+ ndi za akazi awo,+ zoipa zanu ndi za akazi anu,+ zimene munachita m’dziko la Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu?