Yeremiya 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzalanga onse okhala m’dziko la Iguputo monga mmene ndinalangira Yerusalemu. Ndidzawalanga ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+
13 Ndidzalanga onse okhala m’dziko la Iguputo monga mmene ndinalangira Yerusalemu. Ndidzawalanga ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+