Yeremiya 44:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+
29 “Yehova wanena kuti: ‘Tsopano chizindikiro cha zimenezi kwa inu ndi ichi,+ ine ndikulangani m’dziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga adzakwaniritsidwadi moti ndidzakugwetserani tsoka.+