Yeremiya 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mowabu sakutamandidwanso.+ Anthu a ku Hesiboni+ amukonzera chiwembu ndipo akunena kuti: ‘Bwerani amuna inu, tiyeni tifafanize Mowabu kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’+ “Inunso anthu a ku Madimeni khalani chete. Lupanga likukutsatirani.
2 Mowabu sakutamandidwanso.+ Anthu a ku Hesiboni+ amukonzera chiwembu ndipo akunena kuti: ‘Bwerani amuna inu, tiyeni tifafanize Mowabu kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’+ “Inunso anthu a ku Madimeni khalani chete. Lupanga likukutsatirani.