Yeremiya 48:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Muledzeretseni+ anthu inu chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu wadzigwetsa ndipo wagubuduka m’masanzi ake,+ ndipo wakhaladi chinthu chotonzedwa.
26 ‘Muledzeretseni+ anthu inu chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu wadzigwetsa ndipo wagubuduka m’masanzi ake,+ ndipo wakhaladi chinthu chotonzedwa.