Yeremiya 48:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Kodi Isiraeli sanasanduke chinthu chotonzedwa kwa inu?+ Kapena kodi anapezeka pakati pa mbala zenizeni?+ Inu munali kupukusa mitu moipidwa pamene munali kumunenera zinthu zoipa.
27 “‘Kodi Isiraeli sanasanduke chinthu chotonzedwa kwa inu?+ Kapena kodi anapezeka pakati pa mbala zenizeni?+ Inu munali kupukusa mitu moipidwa pamene munali kumunenera zinthu zoipa.