Yeremiya 48:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “‘Inu anthu okhala ku Mowabu, chokani mumzinda ndi kukakhala pathanthwe.+ Khalani ngati njiwa imene imamanga chisa chake pakhomo la dzenje m’matanthwemo.’”+
28 “‘Inu anthu okhala ku Mowabu, chokani mumzinda ndi kukakhala pathanthwe.+ Khalani ngati njiwa imene imamanga chisa chake pakhomo la dzenje m’matanthwemo.’”+