33 Kusangalala ndi kukondwera zachotsedwa m’munda wa zipatso ndiponso m’dziko la Mowabu.+ Ndachititsa kuti vinyo asapezeke moponderamo mphesa.+ Palibe amene adzapondaponda mphesa akufuula mosangalala. Padzamveka kufuula koma osati kwachisangalalo.’”+