Yeremiya 48:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Yehova wanena kuti, ‘Taonani! Monga mmene chiwombankhanga chimatsikira ndi kugwira chakudya chake,+ wina adzatambasula mapiko ake ndi kugwira Mowabu.+
40 “Yehova wanena kuti, ‘Taonani! Monga mmene chiwombankhanga chimatsikira ndi kugwira chakudya chake,+ wina adzatambasula mapiko ake ndi kugwira Mowabu.+