Yeremiya 48:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Matauni adzalandidwa. Malo ake odalirika adzalandidwa. Pa tsikulo, mitima ya amuna amphamvu a ku Mowabu idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.’”+
41 Matauni adzalandidwa. Malo ake odalirika adzalandidwa. Pa tsikulo, mitima ya amuna amphamvu a ku Mowabu idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akumva zowawa za pobereka.’”+