Yeremiya 48:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 M’masiku otsiriza ndidzasonkhanitsa Amowabu onse amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’+ watero Yehova. ‘Apa ndi pamene pathera ziweruzo za Mowabu.’”+
47 M’masiku otsiriza ndidzasonkhanitsa Amowabu onse amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’+ watero Yehova. ‘Apa ndi pamene pathera ziweruzo za Mowabu.’”+