Yeremiya 49:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Pambuyo pake ndidzasonkhanitsa ana a Amoni+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’ watero Yehova.”
6 “‘Pambuyo pake ndidzasonkhanitsa ana a Amoni+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,’ watero Yehova.”