Yeremiya 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndamva uthenga wochokera kwa Yehova ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu a mitundu ina kukanena kuti: “Sonkhanani, muukireni ndi kumuthira nkhondo.”+
14 Ndamva uthenga wochokera kwa Yehova ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu a mitundu ina kukanena kuti: “Sonkhanani, muukireni ndi kumuthira nkhondo.”+