Yeremiya 49:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Thawani, thawirani kutali. Tsikirani kumalo akuya kuti mukakhale kumeneko, inu okhala ku Hazori,”+ watero Yehova. “Pakuti Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ waganiza zokuukirani ndi kukuchitirani zoipa.”
30 “Thawani, thawirani kutali. Tsikirani kumalo akuya kuti mukakhale kumeneko, inu okhala ku Hazori,”+ watero Yehova. “Pakuti Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ waganiza zokuukirani ndi kukuchitirani zoipa.”