Yeremiya 49:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Nyamukani, amuna inu. Pitani kukaukira mtundu wa anthu umene ukukhala mosatekeseka+ ndi mwamtendere!”+ watero Yehova. “Kumeneko kulibe zitseko ndi mipiringidzo. Anthu ake amakhala kwaokhaokha.+
31 “Nyamukani, amuna inu. Pitani kukaukira mtundu wa anthu umene ukukhala mosatekeseka+ ndi mwamtendere!”+ watero Yehova. “Kumeneko kulibe zitseko ndi mipiringidzo. Anthu ake amakhala kwaokhaokha.+