Yeremiya 52:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira,+ ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Libina,+ ndipo dzina lawo linali Hamutali,+ mwana wa Yeremiya.
52 Zedekiya+ anali ndi zaka 21 pamene anayamba kulamulira,+ ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Libina,+ ndipo dzina lawo linali Hamutali,+ mwana wa Yeremiya.